Mtengo Ndi Utumiki Wanu

ebook

By Dag Heward-Mills

cover image of Mtengo Ndi Utumiki Wanu

Sign up to save your library

With an OverDrive account, you can save your favorite libraries for at-a-glance information about availability. Find out more about OverDrive accounts.

   Not today

Find this title in Libby, the library reading app by OverDrive.

Download Libby on the App Store Download Libby on Google Play

Search for a digital library with this title

Title found at these libraries:

Library Name Distance
Loading...

Anthu ambiri samamvetsetsa za malo a mtengo wa dzindikila chabwino ndi choipa m'moyo mwathu. Nthawi zambiri timaganiza kuti unali mtengo qmwe unalipo kalekale munthawi ya Adamu ndi Eva. Timakhulupirira kuti mtengo umeneyo unali ndi zipatso za poizoni zoti ukangodya yemwe wadyayo amafa.
Mwa tsoka, Adamu ndi Eva anadya za mtengowu ndipo anafa. Tikawerenga za nkhaniyi, timaganiza kwa ife, "zinali zomvetsa chisoni Adam ndi Eva kudya chipatso chakuphachi koma tithokoze sitidzaikidwa m'mayeselo ndi mtengo ngati umenewo".
Zachisoni, tikhala tikulimbana ndi mtengo umenewu ndi zipatso zake. Chomwe tiyenera kudziwa ndi chakuti za mtengo wa kudzindikira chabwino ndi choipa udakalipobe mpaka lero. Umagwira ntchito m'mayesero kwa ife chimodzimodzi m'mene unapangira nthawi ya Adamu ndi Eva. Umayimilira ngati njira ina ya kwa Mulungu

Mtengo Ndi Utumiki Wanu