Luso la Utumiki

ebook

By Dag Heward-Mills

cover image of Luso la Utumiki

Sign up to save your library

With an OverDrive account, you can save your favorite libraries for at-a-glance information about availability. Find out more about OverDrive accounts.

   Not today

Find this title in Libby, the library reading app by OverDrive.

Download Libby on the App Store Download Libby on Google Play

Search for a digital library with this title

Title found at these libraries:

Library Name Distance
Loading...

Kukuza luso ndiko kukuza kuthekera. Baibulo limanena kuti kukonderedwa kumadza kwa anthu a luso. Ntchito ya utumiki imafuna kuthekera kwa kukulu.
Bukhu latsopanoli, "Luso la Utumiki" ndi lofunika kwambiri kwa onse amene amakhumbira kuchita ntchito ya Mulungu. Limawonetseratu maganizo omwe ali olondola ndi oipa okhudzana ndi utumiki, chomwe ntchito ya utumiki chiri, chomwe mukuyenera kuchita ngati wogwira ntchito mu utumiki ndi momwe mungapangire ntchito za mtumiki.
Mwadabwapo zokhuzana ndi momwe mungachitire ntchito ya utumiki? Bukhu lapaderali lolembedwa ndi Dag Heward-Mills likakulimbikitsani inu kuyenda moyenereza maitanidwe an a Mulungu ndi kukutsogozani inu mu kudzipereka nokha kwathunthu ku ntchito ya Mulungu.

Luso la Utumiki