Ulaliki Pa Uthenga Wabwino wa Mateyu (II)--Kodi Tinakhulupirira Chiyani Kuti Tilandire Chikhululukiro Cha Machimo?

ebook

By Paul C. Jong

cover image of Ulaliki Pa Uthenga Wabwino wa Mateyu (II)--Kodi Tinakhulupirira Chiyani Kuti Tilandire Chikhululukiro Cha Machimo?

Sign up to save your library

With an OverDrive account, you can save your favorite libraries for at-a-glance information about availability. Find out more about OverDrive accounts.

   Not today

Find this title in Libby, the library reading app by OverDrive.

Download Libby on the App Store Download Libby on Google Play

Search for a digital library with this title

Title found at these libraries:

Library Name Distance
Loading...

Mtumwi Mateyu akutiuza ife kuti Mau a Yesu analankhulidwa kwa aliyense m'dziko lino, popeza Iye ankaona Yesu monga Mfumu ya mafumu. Tsopano, Akristu dziko lonse lapansi, amene angobadwa mwatsopano pokhulupilira mu uthenga wabwino wa madzi ndi Mzimu omwe tikufalitsa, indedi akufunitsitsa kudya mkate wamoyo. Koma ndikobvuta kwa iwo kukhala ndi chiyanjano ndi ife mu uthenga wabwino weni weni, popeza iwo onse ali kutali ndi ife. Choncho, kuti tikumane ndi zofunika zauzimu za anthu amenewa a Yesu Kristu, Mfumu ya mafumu, ulaliki m'buku limeneli wakonzedwa monga mkate watsopano wa moyo kwa iwo kuti usamalire kukula kwao kwauzimu. Mlembi amanena kuti iwo amene alandira chikhululukiro cha machimo ao pokhulupilira m'Mau a Yesu Kristu, Mfumu ya mafumu, ayenera kudya Mau Ake angwiro pofuna kuteteza chikhulupiliro chao komanso kuchita bwino m'miyoyo yao yauzimu. Buku limeneli lidzapereka mkate weni weni wamoyo wauzimu kwa inu nonse amene mwakhala anthu olemekezeka a Mfumu mwa chikhulupiliro. Kudzera mu Mpingo Wake ndi akapolo Ake, Mulungu adzapitiriza kupereka kwa inu mkate umenewu wamoyo. Lolani madalitso a Mulungu akhale pa inu nonse amene mwabadwa mwatsopano mwa madzi ndi Mzimu, amene mukufuna kukhala ndi chiayanjano chauzimu ndi ife mwa Yesu Kristu.

Ulaliki Pa Uthenga Wabwino wa Mateyu (II)--Kodi Tinakhulupirira Chiyani Kuti Tilandire Chikhululukiro Cha Machimo?